Masalimo 78:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anaiwala zochita Iye, ndi zodabwitsa zake zimene anawaonetsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anaiwala zochita Iye, ndi zodabwitsa zake zimene anawaonetsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Iwo adaiŵala zimene Mulungu adachita, ndiponso zozizwitsa zimene Iye adaŵaonetsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Anayiwala zimene Iye anachita, zozizwitsa zimene anawaonetsa. Onani mutuwo |