Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 77:7 - Buku Lopatulika

7 Kodi Ambuye adzataya nthawi yonse? Osabwerezanso kukondwera nafe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Kodi Ambuye adzataya nthawi yonse? Osabwerezanso kukondwera nafe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ndimati, “Kodi Ambuye adzandikana mpaka liti? Kodi sadzandikomeranso mtima?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 “Kodi Ambuye adzatikana mpaka muyaya? Kodi Iwo sadzaonetsanso kukoma mtima kwawo?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 77:7
13 Mawu Ofanana  

Angakhale akagwa, satayikiratu, pakuti Yehova agwira dzanja lake.


Iphani nsembe za chilungamo, ndipo mumkhulupirire Yehova.


Koma mwatitaya, ndi kutinyazitsa; ndipo simutuluka nao makamu a nkhondo athu.


Mulungu, munatitayiranji chitayire? Mkwiyo wanu ufukiranji pa nkhosa za kubusa kwanu?


Yehova, mudzakwiya nthawi zonse kufikira liti? Nidzatentha nsanje yanu ngati moto?


Munachita zovomereza dziko lanu, Yehova; munabweza ukapolo wa Yakobo.


Kodi mudzatikwiyira nthawi zonse? Kodi mudzakhala chikwiyire mibadwomibadwo?


Koma Inu munamtaya, nimunamkaniza, munakwiya naye wodzozedwa wanu.


Mudzabisala kosatha kufikira liti, Yehova; ndi kuzaza kwanu kudzatentha ngati moto kufikira liti?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa