Masalimo 77:4 - Buku Lopatulika4 Mundikhalitsa maso; ndigwidwa mtima wosanena kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Mundikhalitsa maso; ndigwidwa mtima wosanena kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mumagwira zikope zanga kuti ndisagone tulo. Ndikuvutika kwambiri kotero kuti sindingathe kulankhula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Munagwira zikope zanga kuti ndisagone ndipo ndinavutika kwambiri kuti ndiyankhule. Onani mutuwo |