Masalimo 77:1 - Buku Lopatulika1 Ndidzafuulira kwa Mulungu ndi mau anga; kwa Mulungu ndi mau anga, ndipo adzanditcherezera khutu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndidzafuulira kwa Mulungu ndi mau anga; kwa Mulungu ndi mau anga, ndipo adzanditcherezera khutu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ndikulira mopemba kwa Mulungu, ndi mau okweza ndikufuula kwa Mulungu kuti andimve. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndinafuwulira Mulungu kupempha thandizo; ndinafuwula mokweza kwa Mulungu kuti anditcherere khutu. Onani mutuwo |