Masalimo 74:9 - Buku Lopatulika9 Sitiziona zizindikiro zathu; palibenso mneneri; ndipo mwa ife palibe wina wakudziwa mpaka liti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Sitiziona zizindikiro zathu; palibenso mneneri; ndipo mwa ife palibe wina wakudziwa mpaka liti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Zizindikiro zonse za fuko lathu zaonongeka, kulibenso mneneri ndi mmodzi yemwe, palibe ndi mmodzi yemwe pakati pathu amene akudziŵa nthaŵi yodzatha zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ife sitinapatsidwe chizindikiro chodabwitsa; palibe aneneri amene atsala ndipo palibe aliyense wa ife akudziwa kuti izi zidzatenga nthawi yayitali bwanji. Onani mutuwo |