Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 74:10 - Buku Lopatulika

10 Wotsutsanayo adzatonza kufikira liti, Mulungu? Kodi mdani adzanyoza dzina lanu nthawi yonse?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Wotsutsanayo adzatonza kufikira liti, Mulungu? Kodi mdani adzanyoza dzina lanu nthawi yonse?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Inu Mulungu, adani athuŵa adzanyodolabe mpaka liti? Amaliwongowo adzanyozabe dzina lanu mpaka muyaya?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Kodi mpaka liti, mdani adzanyoze Inu Mulungu? Kodi amaliwongowa adzapeputsa dzina lanu kwamuyaya?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 74:10
10 Mawu Ofanana  

Chifukwa cha mau a wotonza wochitira mwano; chifukwa cha mdani ndi wobwezera chilango.


Bwererani Yehova, landitsani moyo wanga; ndipulumutseni chifukwa cha kukoma mtima kwanu.


Ndipo anansi athu amene anatonza Inu muwabwezere chotonza chao, kasanu ndi kawiri kumtima kwao, Ambuye.


Mudzabisala kosatha kufikira liti, Yehova; ndi kuzaza kwanu kudzatentha ngati moto kufikira liti?


Ndani amene, iwe wamtonza ndi kumlalatira? Ndani amene iwe wakwezera mau ako ndi kutukulira maso ako kumwamba? Ndiye Woyera wa Israele.


Ndipo wina anati kwa munthu wovala bafuta, wokhala pamwamba pamadzi a mumtsinje, Chimaliziro cha zodabwitsa izi chidzafika liti?


ndipo anafuula ndi mau aakulu, ndi kunena, Kufikira liti, Mfumu yoyera ndi yoona, muleka kuweruza ndi kubwezera chilango chifukwa cha mwazi wathu, pa iwo akukhala padziko?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa