Masalimo 74:11 - Buku Lopatulika11 Mubwezeranji dzanja lanu, ndilo dzanja lamanja lanu? Mulitulutse kuchifuwa chanu ndipo muwatheretu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Mubwezeranji dzanja lanu, ndilo dzanja lamanja lanu? Mulitulutse kuchifuwa chanu ndipo muwatheretu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Chifukwa chiyani mukubisa dzanja lanu lotithandiza? Bwanji dzanja lanu lamanja likungokhala pachifuwa panu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Chifukwa chiyani mukubweza dzanja lanu lamanja? Litulutseni kuchoka pachifuwa chanu ndipo muwawononge! Onani mutuwo |