Masalimo 74:12 - Buku Lopatulika12 Koma Mulungu ndiye mfumu yanga kuyambira kale, wochita zakupulumutsa pakati padziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma Mulungu ndiye mfumu yanga kuyambira kale, wochita zakupulumutsa pakati pa dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Komabe Inu Mulungu, ndinu mfumu yanga kuyambira kalekale. Ndinu amene mumagwira ntchito yopulumutsa pa dziko lonse lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Koma Inu Mulungu, ndinu Mfumu yanga kuyambira kalekale; Mumabweretsa chipulumutso pa dziko lapansi. Onani mutuwo |