Masalimo 74:13 - Buku Lopatulika13 Mudagawa nyanja ndi mphamvu yanu; mudaswa mitu ya zoopsa za m'madzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Mudagawa nyanja ndi mphamvu yanu; mudaswa mitu ya zoopsa za m'madzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mudagaŵa Nyanja Yofiira ndi mphamvu zanu. Mudaphwanya mitu ya zilombo zam'madzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Ndinu amene munagawa nyanja ndi mphamvu yanu; munathyola mitu ya zirombo za mʼmadzi. Onani mutuwo |