Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 74:14 - Buku Lopatulika

14 Mudaphwanya mitu ya Leviyatani; mudampereka akhale chakudya cha zilombo za m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Mudaphwanya mitu ya Leviyatani; mudampereka akhale chakudya cha zilombo za m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Mudatswanya mitu ya Leviyatani, chilombo cham'madzi chija, nkuitaya kuti ikhale chakudya cha zilombo zam'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Ndinu amene munaphwanya mitu ya Leviyatani ndi kuyipereka ngati chakudya cha zirombo za mʼchipululu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 74:14
9 Mawu Ofanana  

Autemberere iwo akutemberera usana, Odziwa kuutsa Leviyatani.


Okhala m'chipululu adzagwadira pamaso pake; ndi adani ake adzaluma nthaka.


Chomwecho Yehova anapulumutsa Israele tsiku lomwelo m'manja a Aejipito; ndipo Israele anaona Aejipito akufa m'mphepete mwa nyanja.


Tsiku limenelo Yehova ndi lupanga lake lolimba ndi lalikulu ndi lamphamvu adzalanga Leviyatani njoka yothamanga, ndi Leviyatani njoka yopindikapindika; nadzapha ching'ona chimene chili m'nyanja.


Chokhachi musamapikisana naye Yehova, musamaopa anthu a m'dzikomo; pakuti ndiwo mkate wathu; mthunzi wao wawachokera, ndipo Yehova ali nafe; musamawaopa.


Ndipo anagwira chinjoka, njoka yakaleyo, ndiye mdierekezi ndi Satana, nammanga iye zaka chikwi,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa