Masalimo 74:8 - Buku Lopatulika8 Ananena mumtima mwao, Tiwapasule pamodzi; anatentha zosonkhaniramo za Mulungu zonse, m'dzikomo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ananena mumtima mwao, Tiwapasule pamodzi; anatentha zosonkhaniramo za Mulungu zonse, m'dzikomo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mumtima mwao ankati, “Tiyeni tiŵagonjetse kotheratu.” Adatentha malo opatulika onse a Mulungu m'dzikomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ndipo anati mʼmitima yawo, “Tawatha kwathunthu.” Anatentha malo aliwonse amene Mulungu amapembedzedwerako mʼdzikomo. Onani mutuwo |