Masalimo 74:7 - Buku Lopatulika7 Anatentha malo anu opatulika; anaipsa ndi kugwetsa pansi mokhalamo dzina lanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Anatentha malo anu opatulika; anaipsa ndi kugwetsa pansi mokhalamo dzina lanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Nyumba yanu adaitentha, malo amene Inu mumakhalako adaŵaipitsa poŵagwetsera pansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iwo anatentha malo anu opatulika mpaka kuwagwetsa pansi; anadetsa malo okhalamo dzina lanu. Onani mutuwo |