Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 74:6 - Buku Lopatulika

6 Ndipo tsopano aphwanya zosemeka zake zonse ndi nkhwangwa ndi nyundo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo tsopano aphwanya zosemeka zake zonse ndi nkhwangwa ndi nyundo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Pambuyo pake, ndi nsompho ndi nyundo, adakadzula zosemasema zonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Kenaka anaphwanya ndi nkhwangwa ndi akasemasema awo zonse zimene tinapachika.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 74:6
4 Mawu Ofanana  

Ndipo m'kati mwa nyumba munali mikungudza yosemasema, ngati zikho ndi maluwa oti gadaa; munali mikungudza yokhayokha simunaoneke mwala ai.


Nalemba m'makoma onse akuzinga chipinda mafano olemba ngati akerubi ndi migwalangwa ndi maluwa oti gadaa, m'katimo ndi kumbuyo kwake.


Zitseko ziwiri zomwe zinali za mtengo wa azitona, anasemapo ngati akerubi ndi migwalangwa ndi maluwa oti gadaa, nawakuta ndi golide; inde anakutanso ndi golide akerubi ndi migwalangwayo.


Ndipo analembapo ngati akerubi ndi migwalangwa ndi maluwa oti gadaa, nakuta zolembazo ndi golide wopsapsala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa