Masalimo 74:5 - Buku Lopatulika5 Anaoneka ngati osamula nkhwangwa kunkhalango. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Anaoneka ngati osamula nkhwangwa kunkhalango. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Adadulamo zonse, monga momwe anthu amadulira mitengo m'nkhalango. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iwo anachita ngati anthu oti anyamula mbendera zawo kuti adule mitengo mʼnkhalango. Onani mutuwo |
ndiye mwana wa munthu wamkazi wa ana aakazi a Dani, ndipo atate wake ndiye munthu wa ku Tiro, wodziwa kuchita ndi golide, ndi siliva, ndi mkuwa, ndi chitsulo, ndi mwala, ndi mitengo, ndi thonje lofiirira, ndi lamadzi, ndi bafuta la thonje losansitsa ndi lofiira, ndi kuzokota mazokotedwe ali onse, ndi kulingirira chopanga chilichonse; kuti ampatse pokhala pamodzi ndi aluso anu, ndi aluso a mbuye wanga Davide atate wanu.