Masalimo 74:3 - Buku Lopatulika3 Nyamulani mapazi anu kukapenya mapasukidwe osatha, zoipa zonse adazichita mdani m'malo opatulika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Nyamulani mapazi anu kukapenya mapasukidwe osatha, zoipa zonse adazichita mdani m'malo opatulika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Dzayendereni mabwinja oonongeka kwathunthuŵa. Adani aononga zinthu zonse za m'Nyumba yanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tembenuzani mapazi kuloza ku mabwinja awa amuyaya chiwonongeko ichi chonse mdani wabweretsa pa malo opatulika. Onani mutuwo |