Masalimo 74:22 - Buku Lopatulika22 Nyamukani, Mulungu, mudzinenere mlandu nokha; kumbukirani momwe akutonzani wopusa tsiku lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Nyamukani, Mulungu, mudzinenere mlandu nokha; kumbukirani momwe akutonzani wopusa tsiku lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Dzambatukani, Inu Mulungu, tiyeni mudziteteze pa mlandu wanuwo, kumbukirani kuti anthu amwano amakunyodolani tsiku lonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Dzukani Inu Mulungu ndipo dzitetezeni pa mlandu; kumbukirani momwe opusa akukunyozerani tsiku lonse. Onani mutuwo |