Masalimo 74:21 - Buku Lopatulika21 Okhalira mphanthi asabwere nao manyazi; wozunzika ndi waumphawi alemekeze dzina lanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Okhalira mphanthi asabwere nao manyazi; wozunzika ndi waumphawi alemekeze dzina lanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Musalole kuti anthu oponderezedwa achite manyazi. Osauka ndi osoŵa akutamandeni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Musalole kuti osautsidwa abwerere mwamanyazi; osauka ndi osowa atamande dzina lanu. Onani mutuwo |
mudzamvekanso mau akukondwa ndi mau akusekera, mau a mkwati ndi mau a mkwatibwi, mau a iwo akuti, Myamikireni Yehova wa makamu, pakuti Yehova ndiye wabwino, chifundo chake nchosatha; ndi a iwo akutengera nsembe zoyamikira m'nyumba ya Yehova. Pakuti ndidzabweza undende wa dziko monga poyamba, ati Yehova.