Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 74:19 - Buku Lopatulika

19 Musapereke moyo wa njiwa yanu kwa chilombo; musamaiwala moyo wa ozunzika anu nthawi yonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Musapereke moyo wa njiwa yanu kwa chilombo; musamaiwala moyo wa ozunzika anu nthawi yonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Musati mupereke moyo wa nkhunda yanu Israele ku zilombo zakuthengo. Musaiŵale mpaka muyaya moyo wa anthu anu osauka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Musapereke moyo wa nkhunda yanu ku zirombo zakuthengo; nthawi zonse musayiwale miyoyo ya anthu anu osautsidwa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 74:19
12 Mawu Ofanana  

Ukani, Yehova; samulani dzanja lanu, Mulungu; musaiwale ozunzika.


Gulu lanu linakhala m'dziko muja. Mwa ukoma wanu munalikonzera ozunzika, Mulungu.


Pogona inu m'makola a zoweta, mukhala ngati mapiko a njiwa okulira ndi siliva, ndi nthenga zake zokulira ndi golide woyenga wonyezimira.


Potero adzanenera anthu anu mlandu ndi m'chilungamo, ndi ozunzika anu ndi m'chiweruzo.


Pakuti sadzaiwalika nthawi zonse waumphawi, kapena chiyembekezo cha ozunzika sichidzaonongeka kosatha.


Nkhunda yangawe, yokhala m'ming'alu ya thanthwe, mobisika motsetsereka, ndipenye nkhope yako, ndimve mau ako; pakuti mau ako ngokoma, nkhope yako ndi kukongola.


Taona, wakongola, bwenzi langa, namwaliwe, taona, wakongola; maso ako akunga a nkhunda patseri pa chophimba chako. Tsitsi lako likunga gulu la mbuzi, zooneka paphiri la Giliyadi.


Nkhunda yanga, wangwiro wangayu, ndiye mmodzi; ndiye wobadwa yekha wa amake; ndiye wosankhika wa wombala. Ana aakazi anamuona, namutcha wodala; ngakhale akazi aakulu a mfumu, ndi akazi aang'ono namtamanda.


Ndani awa amene auluka ngati mtambo, ndi monga nkhunda kumazenera ao?


Koma ndidzasiya pakati pako anthu ozunzika ndi osauka, ndipo iwo adzakhulupirira dzina la Yehova.


Taonani, Ine ndikutumizani inu monga nkhosa pakati pa mimbulu; chifukwa chake khalani ochenjera monga njoka, ndi oona mtima monga nkhunda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa