Masalimo 73:9 - Buku Lopatulika9 Pakamwa pao anena zam'mwamba, ndipo lilime lao liyendayenda m'dziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakamwa pao anena zam'mwamba, ndipo lilime lao liyendayenda m'dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pakamwa pao pamalankhula monyoza Mulungu kumwamba, ndipo lilime lao ndi losamangika pa dziko lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pakamwa pawo pamayankhula monyoza Mulungu kumwamba ndipo lilime lawo limayenda pa dziko lapansi. Onani mutuwo |
Mukavomereza tsono, pakumva mau a lipenga, chitoliro, zeze, sansi, chisakasa, ndi ngoli, ndi zoimbitsa zilizonse, kugwadira ndi kulambira fano ndinalipanga, chabwino; koma mukapanda kulambira, mudzaponyedwa nthawi yomweyi m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto; ndipo mulungu yemwe adzakulanditsani m'manja mwanga ndani?