Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 73:8 - Buku Lopatulika

8 Achita zaphwete nalankhula moipa za kusautsa, alankhula modzitama.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Achita zaphwete nalankhula moipa za kusautsa, alankhula modzitama.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Amanyodola ndi kumalankhula zoipa, amadzikuza ndi kumaopseza ena kuti, “Tikupsinjani.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Iwowo amanyogodola ndi kumayankhula zoyipa; mwa kudzikuza kwawo amaopseza ena nʼkumati, “Tikuponderezani.”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 73:8
16 Mawu Ofanana  

Itero mfumu, Asakunyengeni Hezekiya; pakuti sadzakhoza kukulanditsani m'dzanja lake;


Podzikuza woipa apsereza waumphawi; agwe m'chiwembu anapanganacho.


Mafuta ao awatsekereza; m'kamwa mwao alankhula modzikuza.


Ndipo pakamwa panu mwadzikuza pa Ine, ndi kundichulukitsira mau anu ndawamva Ine.


Abwerera, koma si kwa Wam'mwambayo; akunga uta wosakhulupirika; akalonga ao adzagwa ndi lupanga mwa chipongwe cha lilime lao; ichi ndicho adzawasekera m'dziko la Ejipito.


koma makamaka iwo akutsata za thupi, m'chilakolako cha zodetsa, napeputsa chilamuliro; osaopa kanthu, otsata chifuniro cha iwo eni, santhunthumira kuchitira mwano akulu aulemerero;


Pakuti polankhula mau otukumuka opanda pake, anyengerera pa zilakolako za thupi, ndi zonyansa, anthu amene adayamba kupulumuka kwa iwo a mayendedwe olakwa;


Amenewo ndiwo odandaula, oderera, akuyenda monga mwa zilakolako zao (ndipo pakamwa pao alankhula zazikuluzikulu), akutama anthu chifukwa cha kupindula nako.


Ndipo m'dziko lonse la Israele simunapezeke wosula; popeza Afilisti adati, Kuti Aisraele angadzisulire malupanga kapena mikondo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa