Masalimo 73:10 - Buku Lopatulika10 Chifukwa chake anthu ake amabwera kudza kuno, ndipo chikho chodzala ndi madzi achigugudiza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Chifukwa chake anthu ake amabwera kudza kuno, ndipo chikho chodzala ndi madzi achigugudiza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Nchifukwa chake ngakhale anthu a Mulungu amabwera kwa iwo, ndipo amakhuta zonena zao ngati madzi akumwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Nʼchifukwa chake anthu awo amapita kwa iwowo ndi kumwa madzi mochuluka. Onani mutuwo |