Masalimo 73:11 - Buku Lopatulika11 Namati, Akachidziwa bwanji Mulungu? Kodi Wam'mwambamwamba ali nayo nzeru? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Namati, Akachidziwa bwanji Mulungu? Kodi Wam'mwambamwamba ali nayo nzeru? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Amati, “Kodi Mulungu angadziŵe bwanji? Kodi Wopambanazonseyo angadziŵe kanthu kalikonse?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Iwo amati, “Kodi Mulungu angadziwe bwanji? Kodi Wammwambamwamba angadziwe kalikonse?” Onani mutuwo |