Masalimo 73:6 - Buku Lopatulika6 Chifukwa chake kudzikuza kunga unyolo pakhosi pao; achivala chiwawa ngati malaya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Chifukwa chake kudzikuza kunga unyolo pakhosi pao; achivala chiwawa ngati malaya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nchifukwa chake amavala kunyada ngati mkanda wam'khosi. Amavala nkhanza ngati malaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Nʼchifukwa chake kunyada kuli monga mkanda wa mʼkhosi mwawo; amadziveka chiwawa. Onani mutuwo |