Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 73:5 - Buku Lopatulika

5 Savutika monga anthu ena; sasautsika monga anthu ena.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Savutika monga anthu ena; sasautsika monga anthu ena.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Saona mavuto monga anthu ena, sazunzika ngati anzao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Saona mavuto monga anthu ena; sazunzika ngati anthu ena onse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 73:5
9 Mawu Ofanana  

Zakuti munthu woipa asungika tsiku la tsoka? Natulutsidwa tsiku la mkwiyo?


Ndikangokumbukira ndivutika mtima, ndi thupi langa lichita nyaunyau.


Nyumba zao sizitekeseka ndi mantha, ngakhale ndodo ya Mulungu siiwakhalira.


Tapenyani, oipa ndi awa; ndipo pokhazikika chikhazikikire aonjezerapo pa chuma chao.


Koma poweruzidwa, tilangidwa ndi Ambuye, kuti tingatsutsidwe pamodzi ndi dziko lapansi.


Koma ngati mukhala opanda chilango, chimene onse adalawako, pamenepo muli am'thengo, si ana ai.


Onse amene ndiwakonda, ndiwadzudzula ndi kuwalanga; potero chita changu, nutembenuke mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa