Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 73:4 - Buku Lopatulika

4 Pakuti palibe zomangira pakufa iwo, ndi mphamvu yao njolimba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Pakuti palibe zomangira pakufa iwo, ndi mphamvu yao njolimba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Iwowo samva kupweteka konse. Matupi ao ndi onenepa ndi athanzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Iwo alibe zosautsa; matupi awo ndi athanzi ndi amphamvu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 73:4
10 Mawu Ofanana  

Popeza anakuta nkhope yake ndi kunenepa kwake, nachita mafunyenye a mafuta m'zuuno zake;


Atsekereza masiku ao ndi zokoma, natsikira m'kamphindi kumanda.


M'mimba mudzamuiwala; mphutsi zidzamudya mokondwera. Sadzamkumbukiranso; ndipo chosalungama chidzathyoledwa ngati mtengo.


Mafuta ao awatsekereza; m'kamwa mwao alankhula modzikuza.


kwa anthu, ndi dzanja lanu, Yehova, kwa anthu a dziko lapansi pano amene cholowa chao chili m'moyo uno, ndipo mimba yao muidzaza ndi chuma chanu chobisika; akhuta mtima ndi ana, nasiyira ana amakanda zochuluka zao.


Pakuti wanzeru saposa chitsiru kukumbukidwa nthawi zonse; pakuti zonse zooneka kale zidzaiwalika m'tsogolomo. Ndipo wanzeru amwalira bwanji ngati chitsirutu.


Ndaona zonsezi masiku anga achabe; pali wolungama angofa m'chilungamo chake, ndipo pali woipa angokhalabe ndi moyo m'kuipa kwake.


Anenepa, anyezimira; inde apitiriza kuchita zoipa; sanenera ana amasiye mlandu wao, kuti apindule; mlandu wa aumphawi saweruza.


Ndipo kunali kuti wopemphayo adafa, ndi kuti anatengedwa iye ndi angelo kunka kuchifuwa cha Abrahamu; ndipo mwini chumayo adafanso, naikidwa m'manda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa