Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 73:21 - Buku Lopatulika

21 Pakuti mtima wanga udawawa, ndipo ndinalaswa mu impso zanga;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Pakuti mtima wanga udawawa, ndipo ndinalaswa m'impso zanga;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Pamene paja ndinkavutika ndi maganizo, ndi kumamva cholasa mumtimamu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Pamene mtima wanga unasautsidwa ndi kuwawidwa mu mzimu mwanga,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 73:21
5 Mawu Ofanana  

Eni mauta ake andizinga, ang'amba impso zanga, osazileka; natsanulira pansi ndulu yanga.


Usavutike mtima chifukwa cha ochita zoipa, usachite nsanje chifukwa cha ochita chosalungama.


Khala chete mwa Yehova, numlindirire Iye; usavutike mtima chifukwa cha iye wolemerera m'njira yake, chifukwa cha munthu wakuchita chiwembu.


Pakuti ndinachitira nsanje odzitamandira, pakuona mtendere wa oipa.


Walasa impso zanga ndi mivi ya m'phodo mwake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa