Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 73:22 - Buku Lopatulika

22 ndinali wam'thengo, wosadziwa kanthu; ndinali ngati nyama pamaso panu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 ndinali wam'thengo, wosadziwa kanthu; ndinali ngati nyama pamaso panu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 ndinali wopusa wosamvetsa kanthu, ndinali ngati chilombo kwa Inu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 ndinali wopusa ndi wosadziwa; ndinali chirombo chopanda nzeru pamaso panu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 73:22
9 Mawu Ofanana  

Tiyesedwa bwanji ngati nyama zakuthengo, ndi kukhala odetsedwa pamaso panu?


Musakhale monga kavalo, kapena ngati bulu, wopanda nzeru; zomangira zao ndizo cham'kamwa ndi chapamutu zakuwakokera, pakuti ukapanda kutero sadzakuyandikiza.


Pakuti aona anzeru amafa, monga aonongekera wopusa, wodyerera momwemo, nasiyira ena chuma chao.


Mulungu, mudziwa kupusa kwanga; ndipo kutsutsika kwanga sikubisikira Inu.


Munthu wopulukira sachidziwa; ndi munthu wopusa sachizindikira ichi;


chakuti pophuka oipa ngati msipu, ndi popindula ochita zopanda pake; chitero kuti adzaonongeke kosatha.


pakuti ndipambana anthu onse kupulukira, ndilibe luntha la munthu.


Ndinati mumtima mwanga, kuti izi zichitika ndi ana a anthu, kuti Mulungu awayese ndi kuti akazindikire eni ake kuti ndiwo nyama zakuthengo.


Ng'ombe idziwa mwini wake, ndi bulu adziwa pomtsekereza: koma Israele sadziwa, anthu anga sazindikira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa