Masalimo 73:20 - Buku Lopatulika20 Monga anthu atauka, apepula loto; momwemo, Inu Ambuye, pakuuka mudzapeputsa chithunzithunzi chao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Monga anthu atauka, apepula loto; momwemo, Inu Ambuye, pakuuka mudzapeputsa chithunzithunzi chao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Inu Ambuye, pamene mudzadzuka mudzaŵanyoza kotheratu, monga momwe munthu amanyozera maloto atadzuka m'maŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Monga loto pamene wina adzuka, kotero pamene Inu muuka, Inu Ambuye, mudzawanyoza ngati maloto chabe. Onani mutuwo |