Masalimo 73:2 - Buku Lopatulika2 Koma ine, ndikadagwa; mapazi anga akadaterereka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma ine, ndikadagwa; mapazi anga akadaterereka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Koma ine ndinali pafupi kuphunthwa, mapazi anga anali pafupi kuterereka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma kunena za ine, mapazi anga anali pafupi kuterereka; ndinatsala pangʼono kugwa. Onani mutuwo |