Masalimo 73:1 - Buku Lopatulika1 Indedi Mulungu achitira Israele zabwino, iwo a mtima wa mbee. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Indedi Mulungu achitira Israele zabwino, iwo a mtima wa mbee. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Zoonadi, Mulungu ndi wabwino kwa olungama, kwa anthu oyera mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mulungu ndi wabwino ndithu kwa Israeli, kwa iwo amene ndi oyera mtima. Onani mutuwo |