Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 73:18 - Buku Lopatulika

18 Indedi muwaika poterera, muwagwetsa kuti muwaononge.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Indedi muwaika poterera, muwagwetsa kuti muwaononge.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Zoonadi, Inu mumapondetsa anthu oipa pa malo oterera. Mumaŵagwetsa mpaka aonongeke.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Zoonadi Inu munawayika pa malo woterera; Mumawagwetsa pansi kuti awonongeke.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 73:18
11 Mawu Ofanana  

Njira yao ikhale ya mdima ndi yoterera, ndipo mngelo wa Yehova awalondole.


Pakuti oipa adzatayika, ndipo adani ake a Yehova adzanga mafuta a anaankhosa; adzanyeka, monga utsi adzakanganuka.


Angakhale akagwa, satayikiratu, pakuti Yehova agwira dzanja lake.


Koma Inu, Mulungu, mudzawatsitsira kudzenje la chionongeko. Anthu okhetsa mwazi ndi achinyengo masiku ao sadzafikira nusu; koma ine ndidzakhulupirira Inu.


chakuti pophuka oipa ngati msipu, ndi popindula ochita zopanda pake; chitero kuti adzaonongeke kosatha.


Koma Inu, Yehova, muli m'mwamba kunthawi yonse.


Ndipo anawabwezera zopanda pake zao, nadzawaononga m'choipa chao; Yehova Mulungu wathu adzawaononga.


Chifukwa chake njira yao idzakhala kwa iwo yonga malo akuterereka m'mdima; adzachotsedwa, nadzagwa momwemo; pakuti ndidzawatengera zoipa, chaka cha kulangidwa kwao, ati Yehova.


Kubwezera chilango nkwanga, kubwezera komwe, pa nyengo ya kuterereka phazi lao; pakuti tsiku la tsoka lao layandika, ndi zinthu zowakonzeratu zifulumira kudza.


amene adzamva chilango, ndicho chionongeko chosatha chowasiyanitsa kunkhope ya Ambuye, ndi kuulemerero wa mphamvu yake,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa