Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 73:17 - Buku Lopatulika

17 mpaka ndinalowa m'zoyera za Mulungu, ndi kulingalira chitsiriziro chao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 mpaka ndinalowa m'zoyera za Mulungu, ndi kulingalira chitsiriziro chao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 mpaka nditakaloŵa m'malo opatulika a Mulungu, apo mpamene ndidaona mathero ake a anthuwo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 kufikira nditalowa mʼmalo opatulika a Mulungu; pamenepo ndinamvetsa mathero awo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 73:17
12 Mawu Ofanana  

Pakuti chiyembekezo cha wonyoza Mulungu nchiyani pomlikhatu Mulungu, pomchotsera moyo wake?


Potsegulira mau anu paunikira; kuzindikiritsa opusa.


Mboni zanu zomwe ndizo zondikondweretsa, ndizo zondipangira nzeru.


Chinthu chimodzi ndinachipempha kwa Yehova, ndidzachilondola ichi, Kuti ndikhalitse m'nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga, kupenya kukongola kwake kwa Yehova ndi kufunsitsa mu Kachisi wake.


Kuti ndione mphamvu yanu ndi ulemerero wanu, monga ndinakuonani m'malo oyera.


Mulungu, m'malo opatulika muli njira yanu; Mulungu wamkulu ndani monga Mulungu?


Koma Inu, Yehova, muli m'mwamba kunthawi yonse.


aneneri anenera monyenga nathandiza ansembe pakulamulira kwao; ndipo anthu anga akonda zotere; ndipo mudzachita chiyani pomalizira pake?


Koma Mulungu anati kwa iye, Wopusa iwe, usiku womwe uno udzafunidwa moyo wako; ndipo zinthu zimene unazikonza zidzakhala za yani?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa