Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 73:14 - Buku Lopatulika

14 Popeza andisautsa tsiku lonse, nandilanga mamawa monse,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Popeza andisautsa tsiku lonse, nandilanga mamawa monse,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Pakuti ndapeza mavuto tsiku lonse, ndipo ndalangidwa m'maŵa mulimonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Tsiku lonse ndapeza mavuto; ndakhala ndi kulangidwa mmawa uliwonse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 73:14
10 Mawu Ofanana  

Mundikonzeranso mboni zonditsutsa, ndi kundichulukitsira mkwiyo wanu; nkhondo yobwerezabwereza yandigwera.


Chikukomerani kodi kungosautsa, kuti mupeputsa ntchito yolemetsa manja anu, ndi kuti muwalira pa uphungu wa oipa?


ndi kuti mucheze naye m'mawa ndi m'mawa, ndi kumuyesa nthawi zonse?


Masautso a wolungama mtima achuluka, koma Yehova amlanditsa mwa onsewa.


Wodala munthu amene mumlanga, Yehova; ndi kumphunzitsa m'chilamulo chanu;


Kupweteka kwanga kuli chipwetekere bwanji, ndi bala langa losapoleka, likana kupola? Kodi mudzakhala kwa ine ngati kamtsinje konyenga, ngati madzi omwerera?


Inu nokha ndinakudziwani mwa mabanja onse a padziko lapansi, m'mwemo ndidzakulangani chifukwa cha mphulupulu zanu zonse.


ndipo mwaiwala dandauliro limene linena nanu monga ndi ana, Mwana wanga, usayese chopepuka kulanga kwa Ambuye, kapena usakomoke podzudzulidwa ndi Iye;


M'menemo mukondwera, kungakhale tsopano kanthawi, ngati kuyenera, mukachitidwe chisoni ndi mayesero a mitundumitundu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa