Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 73:15 - Buku Lopatulika

15 ndikadati, Ndidzafotokozera chotere, taonani, ndikadachita chosakhulupirika ndi mbadwo wa ana ako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 ndikadati, Ndidzafotokozera chotere, taonani, ndikadachita chosakhulupirika ndi mbadwo wa ana ako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Ndikadati, “Ndilankhula monga amachitira iwowo,” ndikadakhala wosakhulupirika kwa zidzukulu zanu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Ndikanati, “Ndidzayankhula motere,” ndikanachita chosakhulupirika kwa ana anu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 73:15
10 Mawu Ofanana  

Pamenepa anaopaopatu, pakuti Mulungu ali mu mbadwo wa wolungama.


Mbumba ya anthu idzamtumikira; kudzanenedwa za Ambuye ku mibadwo yakudza.


Uwu ndi mbadwo wa iwo akufuna Iye, iwo akufuna nkhope yanu, Mulungu wa Yakobo.


Koma inu mwapatuka m'njira; mwakhumudwitsa ambiri m'chilamulo; mwaipsa chipangano cha Levi, ati Yehova wa makamu.


Koma ngati iwe wachititsa mbale wako chisoni ndi chakudya, pamenepo ulibe kuyendayendanso ndi chikondano. Usamuononga ndi chakudya chako, iye amene Khristu adamfera.


Kuli kwabwino kusadya nyama, kapena kusamwa vinyo, kapena kusachita chinthu chilichonse chakukhumudwitsa mbale wako.


Koma inu ndinu mbadwa yosankhika, ansembe achifumu, mtundu woyera mtima, anthu a mwini wake, kotero kuti mukalalikire zoposazo za Iye amene anakuitanani mutuluke mumdima, mulowe kuunika kwake kodabwitsa;


Iai, ana anga, popeza mbiri imene ndilikuimva sili yabwino iai; mulikulakwitsa anthu a Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa