Masalimo 71:4 - Buku Lopatulika4 Ndilanditseni, Mulungu wanga, m'dzanja la woipa, m'dzanja la munthu wosalungama ndi wachiwawa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndilanditseni, Mulungu wanga, m'dzanja la woipa, m'dzanja la munthu wosalungama ndi wachiwawa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Landitseni Inu Mulungu wanga kwa anthu oipa, landitseni ku mphamvu za anthu osalungama ndi ankhalwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Landitseni Inu Mulungu wanga, kuchoka mʼdzanja la oyipa, kuchoka mʼdzanja la oyipa ndi anthu ankhanza. Onani mutuwo |