Masalimo 71:5 - Buku Lopatulika5 Pakuti Inu ndinu chiyembekezo changa, Ambuye Yehova; mwandikhalira wokhulupirika kuyambira ubwana wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakuti Inu ndinu chiyembekezo changa, Ambuye Yehova; mwandikhalira wokhulupirika kuyambira ubwana wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Inu Ambuye, ndinu amene ndimakukhulupirirani, Inu Chauta, ndinu amene ndimakudalirani kuyambira ubwana wanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pakuti Inu mwakhala chiyembekezo changa, Inu Ambuye Wamphamvuzonse, chilimbikitso changa kuyambira ndili mwana. Onani mutuwo |