Masalimo 71:3 - Buku Lopatulika3 Mundikhalire thanthwe lokhalamo, lopitako kosaleka; mwalamulira kundipulumutsa; popeza Inu ndinu thanthwe langa ndi linga langa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Mundikhalire thanthwe lokhalamo, lopitako kosaleka; mwalamulira kundipulumutsa; popeza Inu ndinu thanthwe langa ndi linga langa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mundikhalire thanthwe lothaŵirako, ndiponso linga lolimba lopulumukirako. Inu ndinu thanthwe langa ndi linga langa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mukhale thanthwe langa lothawirapo, kumene ine nditha kupita nthawi zonse; lamulani kuti ndipulumuke, pakuti Inu ndinu thanthwe langa ndi linga langa. Onani mutuwo |