Masalimo 7:8 - Buku Lopatulika8 Yehova aweruza anthu mlandu; mundiweruze, Yehova, monga mwa chilungamo changa, ndi ungwiro wanga uli mwa ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Yehova aweruza anthu mlandu; mundiweruze, Yehova, monga mwa chilungamo changa, ndi ungwiro wanga uli mwa ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Chauta amagamula milandu ya anthu. Tsono thetsani mlandu, Inu Chauta, moyenera, popeza kuti ine sindidalakwe konse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Yehova aweruzeni anthu a mitundu inayo. Ndiweruzeni Yehova, monga mwa chilungamo changa, monga mwa moyo wanga wangwiro, Inu Wammwambamwamba. Onani mutuwo |