Masalimo 7:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo ukuzingeni msonkhano wa anthu; ndipo pamwamba pao mubwerere kunka kumwamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo ukuzingeni msonkhano wa anthu; ndipo pamwamba pao mubwerere kunka kumwamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Musonkhanitse anthu a mitundu yonse pafupi ndi Inu, ndipo muŵaweruze mutakhala pa mpando wanu kumwamba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Lolani gulu la anthu a mitundu ina lisonkhane mokuzungulirani. Alamulireni muli kumwambako; Onani mutuwo |