Masalimo 7:6 - Buku Lopatulika6 Ukani Yehova mu mkwiyo wanu, nyamukani chifukwa cha ukali wa akundisautsa; ndipo mugalamukire ine; mwalamulira chiweruzo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ukani Yehova mu mkwiyo wanu, nyamukani chifukwa cha ukali wa akundisautsa; ndipo mugalamukire ine; mwalamulira chiweruzo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nyamukani, Inu Chauta, muli okwiya, mulimbane ndi adani anga aukali. Dzambatukani, Inu Mulungu wanga, amene mwalamula kuti chilungamo chichitike. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Nyamukani Yehova, mu mkwiyo wanu; nyamukani kutsutsana ndi mkwiyo wa adani anga. Dzukani Mulungu wanga, lamulirani chilungamo chanu. Onani mutuwo |