Masalimo 7:5 - Buku Lopatulika5 mdani alondole moyo wanga, naupeze; naupondereze pansi moyo wanga, naukhalitse ulemu wanga m'fumbi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 mdani alondole moyo wanga, naupeze; naupondereze pansi moyo wanga, naukhalitse ulemu wanga m'fumbi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 mdaniyo andithamangitse ndi kundigwira, andipondereze pansi ndi kundipha, andisiye ndili thasa m'fumbi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 pamenepo lolani adani anga andithamangitse ndi kundipitirira, lolani kuti moyo wanga aupondereze pansi ndipo mundigoneke pa fumbi. Sela Onani mutuwo |