Masalimo 7:14 - Buku Lopatulika14 Taonani, ali m'chikuta cha zopanda pake; anaima ndi chovuta, nabala bodza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Taonani, ali m'chikuta cha zopanda pake; anaima ndi chovuta, nabala bodza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Zoonadi, munthu woipa amalingalira zoipa zokhazokha nthaŵi zonse, ntchito yake ndi kunyenga ndi kuvutitsa anthu ena basi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Taonani, munthu woyipa amalingalira zoyipa zokhazokha nthawi zonse. Zochita zake ndi zosokoneza ndi zovutitsa anthu ena. Onani mutuwo |