Masalimo 7:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo anamkonzera zida za imfa; mivi yake aipanga ikhale yansakali. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo anamkonzera zida za imfa; mivi yake aipanga ikhale yansakali. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Wakonza zida zake zoopsa, waika mivi yamoto ku uta wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mulungu wakonza zida zake zoopsa; Iye wakonzekera mivi yake yoyaka moto. Onani mutuwo |