Masalimo 69:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti changu cha pa nyumba yanu chandidya; ndi zotonza za iwo otonza Inu zandigwera ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti changu cha pa nyumba yanu chandidya; ndi zotonza za iwo otonza Inu zandigwera ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Changu chochitira Nyumba yanu chandiphetsa, chipongwe cha anthu okunyozani chandigwera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 pakuti changu chochitira nyumba yanu chandiphetsa ndipo chipongwe cha iwo amene amanyoza Inu chandigwera. Onani mutuwo |