Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 69:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo ndinalira pa kusala kwa moyo wanga, koma uku kunandikhalira chotonza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo ndinalira pa kusala kwa moyo wanga, koma uku kunandikhalira chotonza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Pamene ndidadzilanga posala zakudya, anthu adandinyoza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Pamene ndikulira ndi kusala kudya, ndiyenera kupirira kunyozedwa;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 69:10
5 Mawu Ofanana  

Changu changa chinandithera, popeza akundisautsa anaiwala mau anu.


Koma ine, pakudwala iwowa, chovala changa ndi chiguduli. Ndinazunza moyo wanga ndi kusala; ndipo pemphero langa linabwera kuchifuwa changa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa