Masalimo 69:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo chovala changa ndinayesa chiguduli, koma amandiphera mwambi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo chovala changa ndinayesa chiguduli, koma amandiphera mwambi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pamene ndidavala chiguduli kuwonetsa chisoni, ndidasanduka chinthu choŵaseketsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 pomwe ndavala chiguduli, anthu amandiseweretsa. Onani mutuwo |