Masalimo 69:12 - Buku Lopatulika12 Okhala pachipata akamba za ine; ndipo oledzera andiimba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Okhala pachipata akamba za ine; ndipo oledzera andiimba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Anthu okhala pa chipata amandinena, ndipo zidakwa zimandiimba nyimbo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iwo amene amakhala pa chipata amandinena, ndipo ine ndine nyimbo ya zidakwa. Onani mutuwo |
koma munadzikweza kutsutsana naye Ambuye wa Kumwamba; ndipo anabwera nazo zotengera za nyumba yake kwa inu; ndi inu ndi akulu anu, akazi anu ndi akazi anu aang'ono, mwamweramo vinyo; mwalemekezanso milungu yasiliva, ndi yagolide, yamkuwa, yachitsulo, yamtengo, ndi yamwala, imene siiona kapena kumva, kapena kudziwa; ndi Mulungu amene m'dzanja mwake muli mpweya wanu, ndi njira zanu zonse, yemweyo simunamchitire ulemu.