Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 69:35 - Buku Lopatulika

35 Pakuti Mulungu adzapulumutsa Ziyoni, nadzamanga mizinda ya Yuda; ndipo iwo adzakhala komweko, likhale laolao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

35 Pakuti Mulungu adzapulumutsa Ziyoni, nadzamanga midzi ya Yuda; ndipo iwo adzakhala komweko, likhale laolao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

35 Mulungu adzapulumutsa Ziyoni, ndipo adzamanganso mizinda ya Yuda. Anthu ake adzakhala kumeneko, ndipo lidzakhala dziko lao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

35 pakuti Mulungu adzapulumutsa Ziyoni ndi kumanganso mizinda ya Yuda, anthu adzakhala kumeneko ndipo dzikolo lidzakhala lawo;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 69:35
17 Mawu Ofanana  

Nyanja ikukume m'kudzala kwake, munda ukondwerere, ndi zonse zili m'mwemo.


Inu mudzauka, ndi kuchitira nsoni Ziyoni; popeza yafika nyengo yakumchitira chifundo, nyengo yoikika.


Pakuti Yehova anamanga Ziyoni, anaoneka mu ulemerero wake;


Ntchito zanu zonse zidzakuyamikani, Yehova; ndi okondedwa anu adzakulemekezani.


Pakamwa panga padzanena chilemekezo cha Yehova; ndi zinthu zonse zilemekeze dzina lake loyera kunthawi za nthawi.


Mlemekezeni, m'mwambamwamba, ndi madzi inu, a pamwamba pa thambo.


Chitirani Ziyoni chokoma monga mwa kukondwera kwanu; mumange malinga a miyala a Yerusalemu.


Ndipo adzayankhanji amithenga a amitundu? Kuti Yehova wakhazikitsa Ziyoni, ndipo m'menemo anthu ake ovutidwa adzaona pobisalira.


Imbani m'mwamba inu, pakuti Yehova wachichita icho; kuwani inu, mbali za pansi padziko; imbani mapiri inu; nkhalango iwe, ndi mitengo yonse m'menemo; chifukwa kuti Yehova wapulumutsa Yakobo, ndipo adzadzilemekezetsa yekha mwa Israele.


Ndine amene ndilimbitsa mau a mtumiki wanga, kuchita uphungu wa amithenga anga; ndi kunena za Yerusalemu, Adzakhalamo anthu; ndi za mizinda ya Yuda; Idzamangidwa; ndipo ndidzautsa malo abwinja ake.


ndiyandikizitsa chifupi chilungamo changa sichidzakhala patali, ndipo chipulumutso changa sichidzachedwa; ndipo ndidzaika chipulumutso m'Ziyoni, cha kwa Israele ulemerero wanga.


Koma m'phiri la Ziyoni mudzakhala opulumuka, ndipo lidzakhala lopatulika; ndi a nyumba ya Yakobo adzakhala nazo zolowa zao.


Ndipo ndinapenya, taonani, Mwanawankhosayo alikuimirira paphiri la Ziyoni, ndipo pamodzi ndi Iye zikwi zana mphambu makumi anai kudza anai, akukhala nalo dzina lake ndi dzina la Atate wake lolembedwa pamphumi pao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa