Masalimo 69:34 - Buku Lopatulika34 Zakumwamba ndi dziko lapansi zimlemekeze, nyanja ndi zonse zoyenda m'mwemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Zakumwamba ndi dziko lapansi zimlemekeze, nyanja ndi zonse zoyenda m'mwemo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Kumwamba ndi pansi pano, nyanja ndi zonse zoyenda m'menemo zitamande Iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Kumwamba ndi dziko lapansi zitamanda Iye, nyanja ndi zonse zomwe zimayenda mʼmenemo, Onani mutuwo |