Masalimo 69:32 - Buku Lopatulika32 Ofatsa anachiona, nakondwera, ndipo inu, ofuna Mulungu, mtima wanu ukhale ndi moyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ofatsa anachiona, nakondwera, ndipo inu, ofuna Mulungu, mtima wanu ukhale ndi moyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Ozunzika aone zimenezo ndipo asangalale, inu amene mumafunafuna Mulungu, mulimbenso mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Wosauka adzaona ndipo adzasangalala, Inu amene mumafunafuna Mulungu, mitima yanu ikhale ndi moyo! Onani mutuwo |